Esitere 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamene anali kukambirana naye zimenezi, nduna za panyumba ya mfumu zinafika, ndipo mofulumira+ zinatenga Hamani ndi kupita naye kuphwando+ limene Esitere anakonza.
14 Pamene anali kukambirana naye zimenezi, nduna za panyumba ya mfumu zinafika, ndipo mofulumira+ zinatenga Hamani ndi kupita naye kuphwando+ limene Esitere anakonza.