Salimo 132:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndithu ndidzadalitsa chakudya chake.+Anthu ake osauka ndidzawapatsa chakudya chokwanira.+ Mateyu 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero onse anadya n’kukhuta, ndipo anatolera zotsala zodzaza madengu 12.+ Maliko 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero anthuwo anadya ndi kukhuta, moti anatolera zotsala zodzaza madengu akuluakulu 7.+