2 Mafumu 4:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Munthuyo atamva zimenezi, anagawira anthuwo chakudyacho. Iwo anadya mpaka chakudyacho chinatsala, mogwirizana ndi mawu a Yehova.+ Maliko 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero anthuwo anadya ndi kukhuta, moti anatolera zotsala zodzaza madengu akuluakulu 7.+ Luka 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho onse anadya ndi kukhuta, ndipo anatolera zotsala kudzaza madengu 12.+ Yohane 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu onsewo atakhuta,+ iye anauza ophunzira ake kuti: “Sonkhanitsani zotsala zonse, kuti pasawonongeke chilichonse.”
44 Munthuyo atamva zimenezi, anagawira anthuwo chakudyacho. Iwo anadya mpaka chakudyacho chinatsala, mogwirizana ndi mawu a Yehova.+
12 Anthu onsewo atakhuta,+ iye anauza ophunzira ake kuti: “Sonkhanitsani zotsala zonse, kuti pasawonongeke chilichonse.”