Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ndi amene akuyenda mosalakwitsa zinthu,+ amene amachita chilungamo,+

      Ndi kulankhula zoona mumtima mwake.+

  • Yesaya 64:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mwabwera kudzathandiza anthu amene akukondwera ndiponso amene akuchita zolungama,+ anthu amene amakukumbukirani potsatira njira zanu.+

      Koma inuyo munakwiya+ chifukwa chakuti ifeyo tinkangopitirizabe kuchimwa+ kwanthawi yaitali. Choncho kodi ndife oyenera kupulumutsidwa?+

  • Machitidwe 24:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pambali imeneyi, ndikuyesetsa mwakhama, kuchita mozindikira+ kuti ndisapalamule kwa Mulungu kapena kwa anthu.

  • Agalatiya 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Choncho tisaleke kuchita zabwino,+ pakuti pa nyengo yake tidzakolola tikapanda kutopa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena