Salimo 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidziwitseni njira zanu, inu Yehova.+Ndiphunzitseni kuyenda m’njira zanu.+ Salimo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Adzachititsa ofatsa kutsatira zigamulo zake,+Ndipo adzaphunzitsa ofatsa kuyenda m’njira yake.+ Hoseya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+
9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+