Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aheberi 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakuti kwenikweni timachita nawo zimene Khristu akuchita,+ ngati zinthu zimene tinali kudalira pa chiyambi, tazigwira mwamphamvu mpaka mapeto.+

  • Aheberi 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndithudi, ganizirani mozama za munthu amene anapirira malankhulidwe onyoza+ ngati amenewo a anthu ochimwa, amene mwa kulankhula koteroko anali kungodzivulaza okha. Ganizirani za munthu ameneyu kuti musatope ndiponso kuti musalefuke.+

  • Chivumbulutso 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi+ adzapitiriza kuponya m’ndende ena a inu, kuti muyesedwe mpaka pamapeto,+ ndipo mudzakhala m’masautso+ masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa,+ ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena