Agalatiya 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho tisaleke kuchita zabwino,+ pakuti pa nyengo yake tidzakolola tikapanda kutopa.+ 2 Atesalonika 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma inu abale, musaleke kuchita zabwino.+