Ezekieli 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Palibe tchimo ngakhale limodzi mwa machimo onse amene anachita limene lidzakumbukiridwe ndi kumulanga nalo.+ Iye anachita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo. Choncho adzakhalabe ndi moyo.’+ Zefaniya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 bwerani kwa Yehova,+ inu nonse ofatsa a padziko lapansi,+ amene mwakhala mukutsatira zigamulo zake. Yesetsani kukhala olungama,+ yesetsani kukhala ofatsa.+ Mwina+ mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+ Machitidwe 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Iye amalandira munthu wochokera mu mtundu uliwonse, amene amamuopa ndi kuchita chilungamo.+
16 Palibe tchimo ngakhale limodzi mwa machimo onse amene anachita limene lidzakumbukiridwe ndi kumulanga nalo.+ Iye anachita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo. Choncho adzakhalabe ndi moyo.’+
3 bwerani kwa Yehova,+ inu nonse ofatsa a padziko lapansi,+ amene mwakhala mukutsatira zigamulo zake. Yesetsani kukhala olungama,+ yesetsani kukhala ofatsa.+ Mwina+ mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+