1 Akorinto 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 chifukwa mukadali anthu oganiza ngati anthu a m’dzikoli.*+ Kodi ngati mukuchitirana nsanje ndi kukangana nokhanokha,+ sindiye kuti ndinu akuthupi ndipo mukuyenda monga anthu?+
3 chifukwa mukadali anthu oganiza ngati anthu a m’dzikoli.*+ Kodi ngati mukuchitirana nsanje ndi kukangana nokhanokha,+ sindiye kuti ndinu akuthupi ndipo mukuyenda monga anthu?+