Miyambo 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Aliyense wopusa amanyoza malangizo* a bambo ake,+ koma munthu aliyense womvera chidzudzulo ndi wochenjera.+ Miyambo 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Wochitira zoipa bambo ake ndiponso wothamangitsa mayi ake,+ ndi mwana wochititsa manyazi ndi wonyozetsa.+ Miyambo 30:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Diso limene limanyoza bambo ake ndiponso limene silimvera mayi ake,+ akhwangwala a kuchigwa* adzalikolowola ndipo ana a chiwombankhanga adzalidya.
5 Aliyense wopusa amanyoza malangizo* a bambo ake,+ koma munthu aliyense womvera chidzudzulo ndi wochenjera.+
26 Wochitira zoipa bambo ake ndiponso wothamangitsa mayi ake,+ ndi mwana wochititsa manyazi ndi wonyozetsa.+
17 Diso limene limanyoza bambo ake ndiponso limene silimvera mayi ake,+ akhwangwala a kuchigwa* adzalikolowola ndipo ana a chiwombankhanga adzalidya.