Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 141:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza kukoma mtima kosatha,+

      Ndipo akandidzudzula ndiye kuti wandidzoza mafuta pamutu panga,+

      Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+

      Pakuti ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.+

  • Miyambo 6:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pakuti lamulolo ndilo nyale,+ ndipo malangizo ndiwo kuwala,+ komanso kudzudzula* kowongola zolakwa ndiko njira yamoyo,+

  • Aheberi 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Zoonadi, palibe chilango chimene chimamveka chosangalatsa pa nthawi yomwe ukuchilandira, koma chimakhala chowawa.+ Komabe pambuyo pake, kwa anthu amene aphunzirapo kanthu pa chilangocho, chimabala chipatso chamtendere,+ chomwe ndi chilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena