Miyambo 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Vinyo ndi wonyoza.+ Chakumwa choledzeretsa chimasokosera+ ndipo aliyense wosochera nacho alibe nzeru.+ Miyambo 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa chidakwa ndiponso munthu wosusuka adzasauka,+ ndipo kuwodzera kudzaveka munthu nsanza.+ Aroma 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tiyeni tiyende moyenera+ monga usana, osati m’maphwando aphokoso ndi kumwa mwauchidakwa,*+ osati m’chiwerewere ndi khalidwe lotayirira,+ ndiponso osati m’mikangano+ ndi nsanje. 1 Akorinto 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 akuba, aumbombo,+ zidakwa,+ olalata, kapena olanda, onsewo sadzalowa mu ufumu wa Mulungu.+ Aefeso 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiponso, musamaledzere naye vinyo,+ mmene muli makhalidwe oipa,+ koma khalanibe odzaza ndi mzimu.+
20 Vinyo ndi wonyoza.+ Chakumwa choledzeretsa chimasokosera+ ndipo aliyense wosochera nacho alibe nzeru.+
13 Tiyeni tiyende moyenera+ monga usana, osati m’maphwando aphokoso ndi kumwa mwauchidakwa,*+ osati m’chiwerewere ndi khalidwe lotayirira,+ ndiponso osati m’mikangano+ ndi nsanje.
18 Ndiponso, musamaledzere naye vinyo,+ mmene muli makhalidwe oipa,+ koma khalanibe odzaza ndi mzimu.+