Habakuku 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Tsoka kwa amene akupatsa anzake chakumwa kuti amwe, koma atachisakaniza ndi mkwiyo ndiponso kupsa mtima kuti anzakewo aledzere+ ndipo iye aone maliseche awo.+
15 “‘Tsoka kwa amene akupatsa anzake chakumwa kuti amwe, koma atachisakaniza ndi mkwiyo ndiponso kupsa mtima kuti anzakewo aledzere+ ndipo iye aone maliseche awo.+