Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 11:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kuwonjezera apo, Davide anamuitana kuti adye ndi kumwa naye pamodzi, ndipo anamuledzeretsa.+ Ngakhale zinali choncho, madzulo Uriya anapita kwa atumiki a mbuye wake kukagona pabedi, ndipo sanapite kunyumba kwake.

  • 2 Samueli 13:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Kenako Abisalomu analamula omutumikira kuti: “Muonetsetse chonde kuti Aminoni akangosangalala mumtima mwake ndi vinyo,+ ine n’kukuuzani kuti, ‘Mukantheni Aminoni!’ pamenepo mumuphe. Musaope.+ Kodi si ndine amene ndakulamulani? Chitani zinthu mwamphamvu ndipo khalani olimba mtima.”

  • Chivumbulutso 17:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 limene mafumu a dziko lapansi anachita nalo dama,+ ndipo linaledzeretsa anthu okhala padziko lapansi ndi vinyo wa dama* lake.”+

  • Chivumbulutso 18:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iye wamwetsa mitundu yonse ya anthu+ vinyo wa mkwiyo, vinyo wa dama lake. Ndipo mafumu a dziko lapansi anachita naye dama.+ Amalonda oyendayenda+ a padziko lapansi analemera chifukwa cha zinthu zambiri zamtengo wapatali zimene mkazi ameneyu anadziunjikira mopanda manyazi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena