1 Samueli 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi yomweyo, Sauli anamulumbirira m’dzina la Yehova kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ sukhala ndi mlandu chifukwa cha nkhani imeneyi!” 1 Samueli 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mfumu inamuuza kuti: “Usachite mantha. Waona chiyani?” Mkaziyo anayankha Sauli kuti: “Ndaona mulungu+ akutuluka m’nthaka.”
10 Nthawi yomweyo, Sauli anamulumbirira m’dzina la Yehova kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ sukhala ndi mlandu chifukwa cha nkhani imeneyi!”
13 Koma mfumu inamuuza kuti: “Usachite mantha. Waona chiyani?” Mkaziyo anayankha Sauli kuti: “Ndaona mulungu+ akutuluka m’nthaka.”