Salimo 82:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ine ndanena kuti, ‘Inu ndinu milungu,+Ndipo nonsenu ndinu ana a Wam’mwambamwamba.+ Yohane 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anawafunsa kuti: “Kodi m’Chilamulo chanu sanalembemo+ kuti, ‘Ine ndinati: “Inu ndinu milungu”’?+
34 Yesu anawafunsa kuti: “Kodi m’Chilamulo chanu sanalembemo+ kuti, ‘Ine ndinati: “Inu ndinu milungu”’?+