20 ndipo aziuza akulu a mzindawo kuti, ‘Mwana wathuyu ndi wosamvera ndiponso ndi wopanduka. Iye samvera mawu athu+ ndipo ndi wosusuka+ ndiponso ndi chidakwa.’+
17 Dziko iwe, ndiwe wodala ngati mfumu yako ili mwana wochokera ku banja lachifumu, ndipo akalonga ako amadya pa nthawi yake kuti akhale amphamvu, osati kumangomwa mopitirira muyezo.+