Mlaliki 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtima wa anthu anzeru umakhala m’nyumba yamaliro,+ koma mtima wa anthu opusa umakhala m’nyumba yachisangalalo.+ Luka 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Patangopita masiku owerengeka, mwana wamng’ono uja anasonkhanitsa zinthu zonse n’kupita kudziko lina lakutali. Kumeneko anasakaza chuma chake chonse mwa kulowerera m’makhalidwe oipa.+ 2 Timoteyo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 achiwembu,+ osamva za ena, odzitukumula ndiponso onyada,+ okonda zosangalatsa, m’malo mokonda Mulungu,+
4 Mtima wa anthu anzeru umakhala m’nyumba yamaliro,+ koma mtima wa anthu opusa umakhala m’nyumba yachisangalalo.+
13 Patangopita masiku owerengeka, mwana wamng’ono uja anasonkhanitsa zinthu zonse n’kupita kudziko lina lakutali. Kumeneko anasakaza chuma chake chonse mwa kulowerera m’makhalidwe oipa.+
4 achiwembu,+ osamva za ena, odzitukumula ndiponso onyada,+ okonda zosangalatsa, m’malo mokonda Mulungu,+