Miyambo 29:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munthu wokonda nzeru amasangalatsa bambo ake,+ koma woyenda ndi mahule amawononga zinthu zamtengo wapatali.+ Luka 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma atangofika mwana wanuyu,+ amene anadya chuma chanu ndi mahule,+ mwamuphera mwana wa ng’ombe wamphongo wonenepa bwino.’+
3 Munthu wokonda nzeru amasangalatsa bambo ake,+ koma woyenda ndi mahule amawononga zinthu zamtengo wapatali.+
30 Koma atangofika mwana wanuyu,+ amene anadya chuma chanu ndi mahule,+ mwamuphera mwana wa ng’ombe wamphongo wonenepa bwino.’+