Miyambo 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Usakhale pakati pa anthu omwa vinyo kwambiri,+ ndiponso pakati pa anthu odya nyama mosusuka.+ Miyambo 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwana womvetsa zinthu amasunga malamulo,+ koma wochita ubwenzi ndi anthu osusuka amachititsa manyazi bambo ake.+
7 Mwana womvetsa zinthu amasunga malamulo,+ koma wochita ubwenzi ndi anthu osusuka amachititsa manyazi bambo ake.+