Miyambo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwana wanga, ukamvera mawu anga+ ndi kusunga malamulo anga ngati chuma chamtengo wapatali,+ Miyambo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwana wanga, usaiwale lamulo langa,+ ndipo mtima wako usunge malamulo anga.+