Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 20:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Vinyo ndi wonyoza.+ Chakumwa choledzeretsa chimasokosera+ ndipo aliyense wosochera nacho alibe nzeru.+

  • Yesaya 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsoka kwa anthu amene amadzuka m’mawa kuti akafunefune chakumwa choledzeretsa.+ Amene amakhala akumwabe mpaka madzulo kutada, moti vinyo amawaledzeretsa.+

  • Aroma 13:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tiyeni tiyende moyenera+ monga usana, osati m’maphwando aphokoso ndi kumwa mwauchidakwa,*+ osati m’chiwerewere ndi khalidwe lotayirira,+ ndiponso osati m’mikangano+ ndi nsanje.

  • 1 Akorinto 10:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndiye chifukwa chake, kaya mukudya kapena kumwa kapena mukuchita china chilichonse, chitani zonse kuti zibweretse ulemerero kwa Mulungu.+

  • 1 Petulo 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti nthawi+ imene yapitayi inali yokwanira kwa inu kuchita chifuniro cha anthu a m’dzikoli+ pamene munali kuchita zinthu zosonyeza khalidwe lotayirira,+ zilakolako zoipa, kumwa vinyo mopitirira muyezo,+ maphwando aphokoso, kumwa kwa mpikisano, ndi kupembedza mafano kosaloleka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena