Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 21:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 “Koma samalani kuti mitima yanu isalemedwe ndi kudya kwambiri, kumwa kwambiri,+ ndi nkhawa+ za moyo, kuti tsikulo lingadzakufikireni modzidzimutsa+

  • Aroma 13:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tiyeni tiyende moyenera+ monga usana, osati m’maphwando aphokoso ndi kumwa mwauchidakwa,*+ osati m’chiwerewere ndi khalidwe lotayirira,+ ndiponso osati m’mikangano+ ndi nsanje.

  • Agalatiya 5:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 kaduka, kumwa mwauchidakwa,*+ maphwando aphokoso, ndi zina zotero. Ponena za zinthu zimenezi, ndikukuchenjezeranitu, ngati mmene ndinachitira poyamba paja, kuti anthu amene amachita zimenezi+ sadzalowa mu ufumu wa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena