Miyambo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ulesi umachititsa tulo tofa nato,+ ndipo munthu waulesi amakhala ndi njala.+ Miyambo 24:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 umphawi wako ndithu udzabwera ngati wachifwamba ndipo kusauka kwako kudzabwera ngati munthu wokhala ndi zida.+
34 umphawi wako ndithu udzabwera ngati wachifwamba ndipo kusauka kwako kudzabwera ngati munthu wokhala ndi zida.+