Miyambo 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi ugonabe mpaka liti, waulesiwe?+ Udzuka nthawi yanji kutulo tako?+ Miyambo 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Usamakonde tulo kuti ungasauke.+ Tsegula maso ako kuti ukhale ndi zakudya zambiri.+ Miyambo 24:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ukati, “Ndigoneko pang’ono, ndibeko katulo pang’ono, ndipindeko manja pang’ono pogona,”+