Miyambo 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwana wozindikira amatuta m’chilimwe. Mwana wochititsa manyazi amakhala ali m’tulo tofa nato pa nthawi yokolola.+ Miyambo 24:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ukati, “Ndigoneko pang’ono, ndibeko katulo pang’ono, ndipindeko manja pang’ono pogona,”+
5 Mwana wozindikira amatuta m’chilimwe. Mwana wochititsa manyazi amakhala ali m’tulo tofa nato pa nthawi yokolola.+