Miyambo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ulesi umachititsa tulo tofa nato,+ ndipo munthu waulesi amakhala ndi njala.+