Miyambo 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wogwira ntchito ndi dzanja laulesi adzakhala wosauka,+ koma dzanja la munthu wakhama ndi limene limalemeretsa.+ Miyambo 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa chidakwa ndiponso munthu wosusuka adzasauka,+ ndipo kuwodzera kudzaveka munthu nsanza.+ Miyambo 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu akakhuta amapondaponda uchi wa kuchisa, koma kwa munthu wanjala chinthu chilichonse chowawa chimatsekemera.+ 2 Atesalonika 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiponso, pamene tinali ndi inu, tinali kukupatsani lamulo ili:+ “Ngati wina sakufuna kugwira ntchito, asadye.”+
4 Wogwira ntchito ndi dzanja laulesi adzakhala wosauka,+ koma dzanja la munthu wakhama ndi limene limalemeretsa.+
7 Munthu akakhuta amapondaponda uchi wa kuchisa, koma kwa munthu wanjala chinthu chilichonse chowawa chimatsekemera.+
10 Ndiponso, pamene tinali ndi inu, tinali kukupatsani lamulo ili:+ “Ngati wina sakufuna kugwira ntchito, asadye.”+