Miyambo 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu akakhuta amakana kudya* uchi wakuchisa,Koma kwa munthu wanjala, ngakhale chinthu chowawa chimatsekemera.
7 Munthu akakhuta amakana kudya* uchi wakuchisa,Koma kwa munthu wanjala, ngakhale chinthu chowawa chimatsekemera.