Miyambo 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu akakhuta amapondaponda uchi wa kuchisa, koma kwa munthu wanjala chinthu chilichonse chowawa chimatsekemera.+
7 Munthu akakhuta amapondaponda uchi wa kuchisa, koma kwa munthu wanjala chinthu chilichonse chowawa chimatsekemera.+