Miyambo 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dzanja la anthu akhama n’limene lidzalamulire,+ koma dzanja laulesi lidzagwira ntchito yaukapolo.+ Miyambo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Waulesi amalakalaka zinthu, chonsecho moyo wake ulibe chilichonse.+ Koma anthu akhama adzanenepa.+ Miyambo 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zolinga za munthu wakhama zimam’pindulira,+ koma aliyense wopupuluma, ndithu adzasauka.+
24 Dzanja la anthu akhama n’limene lidzalamulire,+ koma dzanja laulesi lidzagwira ntchito yaukapolo.+