Miyambo 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapulani a munthu wakhama amamuthandiza kuti zinthu zimuyendere bwino,*+Koma onse amene amachita zinthu mopupuluma amasauka.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:5 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 60 Galamukani!,No. 3 2019, tsa. 10
5 Mapulani a munthu wakhama amamuthandiza kuti zinthu zimuyendere bwino,*+Koma onse amene amachita zinthu mopupuluma amasauka.+