Miyambo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Waulesi amalakalaka zinthu, chonsecho alibe chilichonse.+Koma munthu wakhama zinthu zidzamuyendera bwino.*+
4 Waulesi amalakalaka zinthu, chonsecho alibe chilichonse.+Koma munthu wakhama zinthu zidzamuyendera bwino.*+