1 Mbiri 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana a Yuda anali Ere,+ Onani,+ ndi Shela.+ Mwana wamkazi wa Sua Mkanani ndiye anam’berekera ana atatuwa. Ere mwana woyamba wa Yuda anachita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo iye anamupha.+ Salimo 55:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipa kumanda.+Ndipo anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso anthu achinyengo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+Koma ine ndidzakhulupirira inu.+
3 Ana a Yuda anali Ere,+ Onani,+ ndi Shela.+ Mwana wamkazi wa Sua Mkanani ndiye anam’berekera ana atatuwa. Ere mwana woyamba wa Yuda anachita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo iye anamupha.+
23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipa kumanda.+Ndipo anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso anthu achinyengo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+Koma ine ndidzakhulupirira inu.+