Rute 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo kudzera mwa ana amene Yehova adzakupatsa kwa mtsikanayu,+ nyumba yako ikhale ngati nyumba ya Perezi, amene Tamara anaberekera Yuda.”+ Luka 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 mwana wa Aminadabu,+mwana wa Arini,+mwana wa Hezironi,+mwana wa Perezi,+mwana wa Yuda,+
12 Ndipo kudzera mwa ana amene Yehova adzakupatsa kwa mtsikanayu,+ nyumba yako ikhale ngati nyumba ya Perezi, amene Tamara anaberekera Yuda.”+