Genesis 38:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anaberekanso mwana wina wamwamuna n’kumutcha dzina lakuti Shela. Mwana ameneyu anam’bereka ali ku Akizibu. + Genesis 38:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno Yuda ataziyang’anitsitsa, ananena kuti:+ “Mkaziyu ndi wolungama koposa ine,+ chifukwa sindinam’pereke kwa mwana wanga Shela.”+ Zitatero, Yuda sanagone nayenso.+ 1 Mbiri 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana a Shela+ mwana wa Yuda anali Ere bambo wa Leka, Laada bambo wa Maresha, ndi mabanja a nyumba ya anthu ogwira ntchito yopanga nsalu zabwino kwambiri,+ a nyumba ya Asibeya,
5 Anaberekanso mwana wina wamwamuna n’kumutcha dzina lakuti Shela. Mwana ameneyu anam’bereka ali ku Akizibu. +
26 Ndiyeno Yuda ataziyang’anitsitsa, ananena kuti:+ “Mkaziyu ndi wolungama koposa ine,+ chifukwa sindinam’pereke kwa mwana wanga Shela.”+ Zitatero, Yuda sanagone nayenso.+
21 Ana a Shela+ mwana wa Yuda anali Ere bambo wa Leka, Laada bambo wa Maresha, ndi mabanja a nyumba ya anthu ogwira ntchito yopanga nsalu zabwino kwambiri,+ a nyumba ya Asibeya,