1 Mbiri 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Davide, Alevi onse onyamula Likasa, oimba, ndi Kenaniya+ mtsogoleri pa ntchito yonyamula katundu imene oimba+ anali kugwira, anavala malaya akunja odula manja, ansalu yabwino kwambiri. Koma Davide anavalanso efodi+ wansalu. 2 Mbiri 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anapanganso nsalu yotchinga+ ya ulusi wabuluu,+ ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira ndi nsalu yofiira komanso yabwino kwambiri. Kenako nsaluyo anaikongoletsa ndi akerubi.+
27 Davide, Alevi onse onyamula Likasa, oimba, ndi Kenaniya+ mtsogoleri pa ntchito yonyamula katundu imene oimba+ anali kugwira, anavala malaya akunja odula manja, ansalu yabwino kwambiri. Koma Davide anavalanso efodi+ wansalu.
14 Anapanganso nsalu yotchinga+ ya ulusi wabuluu,+ ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira ndi nsalu yofiira komanso yabwino kwambiri. Kenako nsaluyo anaikongoletsa ndi akerubi.+