Salimo 60:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Giliyadi ndi wanga, ngati mmene zilili ndi Manase,+Ndipo Efuraimu ndi chipewa choteteza* mutu wanga.Yuda akuimira mphamvu zanga zolamula.+
7 Giliyadi ndi wanga, ngati mmene zilili ndi Manase,+Ndipo Efuraimu ndi chipewa choteteza* mutu wanga.Yuda akuimira mphamvu zanga zolamula.+