Salimo 60:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Giliyadi ndi wanga ndipo Manase ndi wanganso.+Efuraimu ndi malo otetezeka a mtsogoleri amene ine ndamuika.Yuda ndi ndodo ya mtsogoleri wanga.+
7 Giliyadi ndi wanga ndipo Manase ndi wanganso.+Efuraimu ndi malo otetezeka a mtsogoleri amene ine ndamuika.Yuda ndi ndodo ya mtsogoleri wanga.+