Salimo 87:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndidzatchula Rahabi*+ ndi Babulo+ monga ena mwa amene akundidziwa.Ponena za Filisitiya,+ Turo ndi Kusi ine ndidzati:“Amenewa anabadwira m’Ziyoni.”+ Salimo 89:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwaphwanya Rahabi*+ ndi kumuchititsa kukhala ngati munthu amene waphedwa.+Mwabalalitsa adani anu ndi dzanja lanu lamphamvu.+
4 Ine ndidzatchula Rahabi*+ ndi Babulo+ monga ena mwa amene akundidziwa.Ponena za Filisitiya,+ Turo ndi Kusi ine ndidzati:“Amenewa anabadwira m’Ziyoni.”+
10 Mwaphwanya Rahabi*+ ndi kumuchititsa kukhala ngati munthu amene waphedwa.+Mwabalalitsa adani anu ndi dzanja lanu lamphamvu.+