Salimo 85:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi mutikwiyira mpaka kalekale?+ Kodi mudzapitiriza kusonyeza mkwiyo wanu ku mibadwomibadwo?