Yesaya 45:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Isiraeli adzapulumutsidwa chifukwa chokhala pa mgwirizano ndi Yehova+ ndipo adzakhala wopulumutsidwa mpaka kalekale.+ Anthu inu simudzachita manyazi+ ndipo simudzanyozeka+ mpaka kalekale, ngakhale kwamuyaya. Yeremiya 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu amene amandizunza achite manyazi+ koma musalole kuti ineyo ndichite manyazi.+ Anthuwo agwidwe ndi mantha aakulu koma musalole kuti ine ndigwidwe ndi mantha aakulu. Agwetsereni tsoka+ ndipo muwaphwanye kuwirikiza kawiri.+
17 Koma Isiraeli adzapulumutsidwa chifukwa chokhala pa mgwirizano ndi Yehova+ ndipo adzakhala wopulumutsidwa mpaka kalekale.+ Anthu inu simudzachita manyazi+ ndipo simudzanyozeka+ mpaka kalekale, ngakhale kwamuyaya.
18 Anthu amene amandizunza achite manyazi+ koma musalole kuti ineyo ndichite manyazi.+ Anthuwo agwidwe ndi mantha aakulu koma musalole kuti ine ndigwidwe ndi mantha aakulu. Agwetsereni tsoka+ ndipo muwaphwanye kuwirikiza kawiri.+