Salimo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye wokhala kumwamba+ adzaseka,Yehova adzawanyodola.+ Salimo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+Yehova, mpando wake wachifumu uli kumwamba.+Maso ake amaona, maso ake owala amasanthula+ ana a anthu. Salimo 115:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Mulungu wathu ali kumwamba.+Chilichonse chimene anafuna kuchita anachita.+ Mateyu 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Koma inu muzipemphera motere:+ “‘Atate wathu wakumwamba, dzina+ lanu liyeretsedwe.+
4 Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+Yehova, mpando wake wachifumu uli kumwamba.+Maso ake amaona, maso ake owala amasanthula+ ana a anthu.