2 Mbiri 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Mulungu wathu kodi simuwaweruza?+ Ifeyo patokha tilibe mphamvu zotha kulimbana ndi khamu lalikulu limene likubwera kudzamenyana nafeli+ ndipo sitikudziwa chochita,+ koma maso athu ali pa inu.”+ Salimo 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso anga amayang’ana kwa Yehova nthawi zonse,+Chifukwa iye ndi amene amawonjola phazi langa mu ukonde.+ Salimo 123:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 123 Ndakweza maso anga kuyang’ana inu,+Kuyang’ana inu amene mukukhala kumwamba.+
12 Inu Mulungu wathu kodi simuwaweruza?+ Ifeyo patokha tilibe mphamvu zotha kulimbana ndi khamu lalikulu limene likubwera kudzamenyana nafeli+ ndipo sitikudziwa chochita,+ koma maso athu ali pa inu.”+
15 Maso anga amayang’ana kwa Yehova nthawi zonse,+Chifukwa iye ndi amene amawonjola phazi langa mu ukonde.+