Luka 12:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiye Ambuye ananena kuti: “Ndi ndani kwenikweni amene ndi mtumiki woyangʼanira nyumba wokhulupirika komanso wanzeru, amene mbuye wake adzamuike kuti aziyangʼanira gulu la atumiki ake,* kuti aziwapatsa chakudya chokwanira pa nthawi yoyenera?+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:42 Yesu—Ndi Njira, tsa. 182 Nsanja ya Olonda,7/15/2013, tsa. 204/15/2011, tsa. 46/15/2009, ptsa. 20-214/1/2007, ptsa. 22-233/15/1990, ptsa. 10-11, 15-1610/1/1988, tsa. 9
42 Ndiye Ambuye ananena kuti: “Ndi ndani kwenikweni amene ndi mtumiki woyangʼanira nyumba wokhulupirika komanso wanzeru, amene mbuye wake adzamuike kuti aziyangʼanira gulu la atumiki ake,* kuti aziwapatsa chakudya chokwanira pa nthawi yoyenera?+
12:42 Yesu—Ndi Njira, tsa. 182 Nsanja ya Olonda,7/15/2013, tsa. 204/15/2011, tsa. 46/15/2009, ptsa. 20-214/1/2007, ptsa. 22-233/15/1990, ptsa. 10-11, 15-1610/1/1988, tsa. 9