Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 34:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mikango yamphamvu ingakhale ndi chakudya chochepa ndipo ingamve njala.+

      Koma ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+

  • Salimo 37:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndinali mwana, ndipo tsopano ndakula,+

      Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+

      Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+

  • Malaki 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndithu, anthu inu mudzaonanso kusiyana pakati pa munthu wolungama ndi woipa+ ndiponso pakati pa munthu amene akutumikira Mulungu ndi amene sanatumikirepo Mulungu.”+

  • Luka 16:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma Abulahamu anati, ‘Mwanawe, kumbukira kuti unalandiriratu zabwino zako zonse pamene unali moyo, ndipo Lazaro analandiriratu zinthu zoipa. Koma tsopano akusangalala kuno ndipo iwe ukuzunzika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena