Salimo 58:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo mtundu wa anthu udzati:+ “Ndithudi wolungama adzalandira mphoto.+Ndithudi pali Mulungu amene akuweruza dziko lapansi.”+ Aroma 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaweruza aliyense malinga ndi ntchito zake motere:+
11 Ndipo mtundu wa anthu udzati:+ “Ndithudi wolungama adzalandira mphoto.+Ndithudi pali Mulungu amene akuweruza dziko lapansi.”+