-
Luka 16:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Koma Abulahamu anati, ‘Mwanawe, kumbukira kuti unalandiriratu zabwino zako zonse pamene unali moyo, ndipo Lazaro analandira zinthu zoipa. Ndiye panopa akusangalala kuno koma iwe ukuzunzika.
-