Luka 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Abulahamu anati, ‘Mwanawe, kumbukira kuti unalandiriratu zabwino zako zonse pamene unali moyo, ndipo Lazaro analandiriratu zinthu zoipa. Koma tsopano akusangalala kuno ndipo iwe ukuzunzika.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:25 Yesu—Ndi Njira, tsa. 209
25 Koma Abulahamu anati, ‘Mwanawe, kumbukira kuti unalandiriratu zabwino zako zonse pamene unali moyo, ndipo Lazaro analandiriratu zinthu zoipa. Koma tsopano akusangalala kuno ndipo iwe ukuzunzika.+