Salimo 72:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti adzalanditsa wosauka amene akufuula popempha thandizo,+Komanso wosautsika ndi aliyense wopanda womuthandiza.+ Danieli 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 inde, pamene ndinali kulankhula zimenezi m’pemphero, munthu uja Gabirieli,+ amene ndinamuona m’masomphenya nditatopa kwambiri poyamba paja,+ ndinamuona akubwera kwa ine pa nthawi yopereka nsembe yamadzulo, yoperekedwa ngati mphatso.+
12 Pakuti adzalanditsa wosauka amene akufuula popempha thandizo,+Komanso wosautsika ndi aliyense wopanda womuthandiza.+
21 inde, pamene ndinali kulankhula zimenezi m’pemphero, munthu uja Gabirieli,+ amene ndinamuona m’masomphenya nditatopa kwambiri poyamba paja,+ ndinamuona akubwera kwa ine pa nthawi yopereka nsembe yamadzulo, yoperekedwa ngati mphatso.+